Makina Okumbira Misewu Ndi Zinthu Zina

SiteID: 9
Category: C
lnggcode: ny
id:11

KOBELCO EXCAVATOR SK75SR-3

ECO-mode yatsopano mu SK75SR imachititsa kuti izimwa mafuta ochepa pofuna kutembenuza ma SR model kuti akhale makina apamwamba kwambiri.

المواصفات :

 • Ntchito Zomwe Amagwira: 56 hp
 • Ma Engine: 6,940 kg
 • Kulemera: 0.28㎥ bucket
 • Range: Mini
 • Hydraulic System: Two variable displacement pumps + 1 gear pump
 • Kayendedwe: 2 x axial piston, two-speed motors

KOBELCO EXCAVATOR SK210HDLC

Pogwiritsa ntchito ukadaula wawo,a KOBELCO anapanga SK210DHL, yomwe ndi excavator yanyuwani yomwe ndiyoyenerana ndi ukadaulo wantchito ya zomangamanga. Kapangidwe katsopanoka kamabweretsa zinthu zina zachilendo zabwino ku ntchito ya zomangamanga.

المواصفات :

 • Ntchito Zomwe Amagwira: 158 hp
 • Ma Engine: 21,400KG
 • Kulemera: 0.8 m3 ISO heaped
 • Range: Medium
 • Hydraulic System: Two variable displacement pumps + 1 gear pump
 • Kayendedwe: 2 X axial-piston, two-step motors

KOBELCO EXCAVATOR SK250

Popita patsogolo ndi luso la technology, a KOBELCO adakonza ma SK series omwe ndi ma excavator amakono omwe amafikira zofuna za ma kampani ambiri a zomangamanga.Makinawa abweretsa kapangidwe ka makono ka zinthu mmalinga ndi momwe adapangidwira.

المواصفات :

 • Ntchito Zomwe Amagwira: 184 hp
 • Ma Engine: 24,600KG
 • Kulemera: 0.81 – 1.4 m3 ISO heaped
 • Range: Medium
 • Hydraulic System: Two variable displacement pumps + 1 gear pump
 • Kayendedwe: 2 X axial-piston, two-step motors

KOBELCO EXCAVATOR SK260LC

Pogwiritsa ntchito ukadaulo wawo onse iwowa anakonzanso ma SK series, excavator yatsopano yomwe inapangidwa mamakono moyenerana ndi zofuna za makampani a zomangamanga.

المواصفات :

 • Ntchito Zomwe Amagwira: 184 hp
 • Ma Engine: 25,200KG
 • Kulemera: 0.81 – 1.4 m3 ISO heaped
 • Range: Long Reach
 • Hydraulic System: Two variable displacement pumps + 1 gear pump
 • Kayendedwe: 2 X axial-piston, two-step motors

KOBELCO EXCAVATOR SK330

Pogwiritsa ntchito ukadaulo wawo onse iwowa anakonzanso ma SK series, excavator yatsopano yomwe inapangidwa mamakono moyenerana ndi zofuna za makampani a zomangamanga.

المواصفات :

 • Ntchito Zomwe Amagwira: 280 hp
 • Ma Engine: 33,700KG
 • Kulemera: 1.2 – 2.3 m3 ISO heaped
 • Range: Medium
 • Hydraulic System: wo variable displacement pumps + 1 gear pump
 • Kayendedwe: 2 X axial-piston, two-step motors

KOBELCO EXCAVATORS SK380HDLC

Pogwiritsa ntchito ukadaulo wawo,a KOBELCO anapanga SK210DHL, yomwe ndi excavator yanyuwani yomwe ndiyoyenerana ndi ukadaulo wa ntchito ya zomangamanga. Kapangidwe katsopano ka kamabweretsa zinthu zina zachilendo zabwino ku ntchito ya zomangamanga.

المواصفات :

 • Ntchito Zomwe Amagwira: 280 hp
 • Ma Engine: 35,800KG
 • Kulemera: 1.4 - 2.3 m3 ISO heaped
 • Range: Medium
 • Hydraulic System: Two variable displacement pumps + 1 gear pump
 • Kayendedwe: 2 X axial-piston, two-step motors

KOBELCO EXCAVATORS SK500HDLC

Makina a ACERA GEOSPEC a kampani ya KOBELCO ndi atsopano ndipo amafikira ndikukwaniritsa zofuna za makasitomala ambiri. Iwowa akuti amapanga makina atsopano amayang`ana kwambiri zinthu zomwe anthu akufuna. Ngakhale amkafuna kupanga makina omwe angakwanitse kukumba mosavuta, Iwowa anawonetsetsanso kuti makinawa akumwa mafuta moyenerera.

المواصفات :

 • Ntchito Zomwe Amagwira: 344 hp
 • Ma Engine: 51,900 kg
 • Kulemera: 2.1 - 3.4 m3 ISO heaped
 • Range: Large
 • Hydraulic System: Two variable displacement pumps + 1 gear pump
 • Kayendedwe: 2 X axial-piston motor, two-step motors

KOBELCO EXCAVATOR SK850LC

Ma Excavator awa amakwaniritsa ntchito yonse yomwe ingagwiridwe ndi Excavator yayikulu. Tsopano,kwabadwa makina atsopano 80-ton ACERA GEOSPEC SK850LC omwe amagwira ntchito moyenerera.

المواصفات :

 • Ntchito Zomwe Amagwira: 496 hp
 • Ma Engine: 78,200 kg – 80,500 kg
 • Kulemera: 2.8 – 5.4 m3 ISO heaped
 • Range: Large
 • Hydraulic System: Two variable displacement pumps + 1 gear pump
 • Kayendedwe: 2 X axial-piston, two-step motors

KOBELCO EXCAVATOR SK55SRX

Makono, kampani ya KOBELCO ikuwonjezera mphamvu pa makina ake ndipo papangidwa makina ena a SK55SRX omwe ali a mphamvu ndiwodalirika kwambiri.

المواصفات :

 • Ntchito Zomwe Amagwira: 37.4 hp
 • Ma Engine: 5,130 kg
 • Kulemera: 0.21 cu.yd 0.16 m3
 • Range: Mini
 • Hydraulic System: Two variable displacement pumps + 1 gear pump
 • Kayendedwe: 2 X axial-piston, two-step motors

KOBELCO EXCAVATOR SK210LC

Ma excavator awa adapangidwa ndi luso la pamwamba zomwe zimachititsa kuti akhale oyenerana ndi malo omwe akugwirapo ntchito ndikugwira ntchitoyo moyenerera Ma Excavator a mbambande a KOBELCO abwera.

المواصفات :

 • Ntchito Zomwe Amagwira: 157 hp
 • Ma Engine: 22,000KG
 • Kulemera: 0.92 - 1.22 cu.yd. SAE
 • Range: Long Reach
 • Hydraulic System: Two variable displacement pumps + 1 gear pump
 • Kayendedwe: 2 X axial-piston, two-step motors