KOBELCO EXCAVATOR SK260LC

Fomu yofunsira

Pogwiritsa ntchito ukadaulo wawo onse iwowa anakonzanso ma SK series, excavator yatsopano yomwe  inapangidwa mamakono moyenerana ndi zofuna za makampani a zomangamanga.

Atakhala pansi pofuna kupanga ma excavator a atsopano a hydraulic,a KOBELCO  anaganizira zopanga makina a mphamvu zambiri kuti azigwira ntchito mosavuta koma pa nthawi yomweyo anawonetsetsanso kuti kamwedwe ka mafuta kali bwino mosapereka chiopsezo chirichonse ku zinthu zozungilira

Pogwiritsa ntchito ukadaulo wawo onse iwowa anakonzanso ma SK series, excavator yatsopano yomwe  inapangidwa mamakono moyenerana ndi zofuna za makampani a zomangamanga 

المواصفات :

  • Ntchito Zomwe Amagwira : 184 hp
  • Ma Engine : 25,200KG
  • Kulemera : 0.81 – 1.4 m3 ISO heaped
  • Range : Long Reach
  • Hydraulic System : Two variable displacement pumps + 1 gear pump
  • Kayendedwe : 2 X axial-piston, two-step motors