KOBELCO EXCAVATOR SK250

Fomu yofunsira

Popita patsogolo ndi luso la technology, a KOBELCO adakonza ma SK series omwe ndi ma excavator amakono omwe amafikira zofuna za ma kampani ambiri a zomangamanga.Makinawa  abweretsa kapangidwe ka makono ka zinthu mmalinga ndi momwe adapangidwira.

Atakhala pansi pofuna kupanga ma excavator a atsopano a hydraulic,a KOBELCO  anaganizira zopanga makina a mphamvu zambiri kuti azigwira ntchito mosavuta koma pa nthawi yomweyo anawonetsetsanso kuti kamwedwe ka mafuta kali bwino mosapereka chiopsezo chirichonse ku zinthu zozungilira.

المواصفات :

  • Ntchito Zomwe Amagwira : 184 hp
  • Ma Engine : 24,600KG
  • Kulemera : 0.81 – 1.4 m3 ISO heaped
  • Range : Medium
  • Hydraulic System : Two variable displacement pumps + 1 gear pump
  • Kayendedwe : 2 X axial-piston, two-step motors