KOBELCO EXCAVATOR SK210LC

Fomu yofunsira

Ma excavator awa adapangidwa ndi luso la pamwamba  zomwe zimachititsa kuti akhale oyenerana ndi malo omwe akugwirapo ntchito ndikugwira ntchitoyo moyenerera

Ma Excavator a mbambande a KOBELCO abwera.

Awa ndi makina omwe amatha kukumba  malo aliwonse mosavuta chifukwa ndi a mphamvu kwambiri. Iwowa ali ndi ma engine a Hino yomwe ndiyodalirika kwambiri.

Makina a Kobelco anapangidwa kwa zaka zochuluka ndipo ali ndikuthekera konse kokwaniritsa zofuna za owagulitsa ntchito.

المواصفات :

  • Ntchito Zomwe Amagwira : 157 hp
  • Ma Engine : 22,000KG
  • Kulemera : 0.92 - 1.22 cu.yd. SAE
  • Range : Long Reach
  • Hydraulic System : Two variable displacement pumps + 1 gear pump
  • Kayendedwe : 2 X axial-piston, two-step motors