Fomu yofunsira
Makina abwino osavuta kugwiritsa ntchito
Makina a Case TX telescopic handler ndi abwino kwambir kamba koti anawapanga moti anthu adzitha kuwagwiritsa ntchito mosavuta.
KUFIKIRA MALO APATALI
Makina amafikira mpaka pa mtunda wa ma mita khumi , asanu ndi awiri(17) ndipo ndiwodalirika kuti sangathe kugwetsa kapena kuwononga katundu.
MPHAMVU
Makina a TX Telehandler ali ndi ma engine a mphamvu omwe samamwa mafuta kwambiri. Kupatula kuti makinawa samwa mafuta ambiri, ubwino wina ndiwoti ali ndi 516 Nm ya torque yomwe ndiyokwanira kunyamula katundu aliyense mu nyengo iliyonse.