SOIL COMPACTOR

Fomu yofunsira

ACHANGU POGWIRITSA NTCHITO

-Ili ndi ma frequency ofanana komanso amplitude mu vibration

-Ili ndi Cross-bar yomwe imathandiza kupereka mphamvu ku makinawa

NDIWOPHWEKA KOMANSO SAPEREKA CHIOPSYEZO KWA OWAGWIRITSA NTCHITO

Makinawa ndi osavuta kugwiritsa ntchito komanso kuti munthu akamagwiritsa ntchito sakhala ndi nkhawa iliyonse kamba koti makinawa ali ndiwosaopsya kwa owagwiritsa ntchito

AMAGWIRA NTCHITO MOYENERERA

Engine ya makinawa ili ndi  system yomwe imachulukitsa mpweya olowa womwe umathandiza kuti makinawa agwire ntchito moyenerera komanso kuchipetsa kamwedwe ka mafuta

NDIWOSAOPSA KUGWIRITSA NTCHITO KOMANSO WOSAVUTA KUKONZETSA AKAWONONGEKA

Makinawa ndiwosavuta kukonza kamba koti sasowa ukadawulo wambiri kuti atheke zomwe zimachepetsa ndalama zowonongedwa pokonzetsa makinawa.

HIGH RELIABILITY

Makinawa  ali ndi zipangizo zina monga drum shell yomwe imapereka resistance komanso kufanana kwa ntchito yomwe ikugwiridwa.

المواصفات :

  • Kapangidwe : 1107 DX
  • Engine : FPT S8000 TIER 3
  • Mphamvu : 105 hp
  • Kulemera (kg) : 10810