Fomu yofunsira
Kukula mu mphamvu,Kukula mu ufulu
Ntchito ingakule bwanji, a Case ali ndi makina omwe angathe kunyamula katundu wanu mosavuta. Makina awo atsopano omwe apanga ndi ali ndi zinthu izi:
- Mphamvu zambiri
- Ndiwokhazikika bwinobwino
- Ndiwosavuta kugwiritsa ntchito
- Ndi amakono komanso apamwamba kwambiri
Ili ndi zinthu zina zambiri zowonjezera zomwe sizipezeka mu makina ena
Kuwonjezera kwa zipangizo zina
Monga tanenera mwambamu a Case Construction awonjezera ma Skid Steer Loader ndipo tsopano ali ndi radil lift SR boom skid steers komanso vertical lift SV models
Kupanga makina obweretsa mphamvu kuchokera mchaka cha 1969
Kuchokera pomwe anapanga makina awo oyamba otchedwa 1530 Uni-Loader, Kampani ya Case yakhala ikudziwika bwino kwambiri pa ntchito yopanga makina obweretsa mphamvu odalirika. Izi zakhala zikutheka kamba koti kampaniyi inawonjezera zinthu zatsopano pamakina awo monga ma Ride Control komanso nyali zowonjezera.