Fomu yofunsira
Kukula kwa msika wa kampani ya Case
Makina a makono a 570T amachititsa kuti ntchito izitheka mwachangu komanso ndiwodalirika kwambiri. Makinawa achititsa kuti msika wa kampani ya Case ukule kamba koti anthu ambiri mmayiko osiyanasiyana amakonda kugwiritsa ntchito makinawa
“S-tyled backhoe”
Makina atsopano a Backhoe akupitiriza ntchito yabwino yomwe kampani ya Case imadziwika nayo
Engine za S800 kuchokera kwa akatswiri popanga engine padziko lonse
Kampani ya FPT yomwe imapanga ma engine 600,000 pa chaka, ndiyayikulu kwambiri pa makampani onse opanga ma engine. Izi ziri chonchi chifukwa choti kampaniyi yapita pa tsogolo kwambiri pankhani ya technology ndipo ma engine ake ndiwodalirika komanso osaboola mnthumba akawonongeka.
Makina opakilira katundu
Makina opakilira katundu a kampani ya Case ndi apamwamba ndipo anthu amawakonda chifukwa amatha kufikira mulingo uliwonse . Makinawa ndiwosavuta kugwiritsa ntchito chifukwa choti amatha kufikira malo ena aliwonse pawokha.