CASE TELESCOPIC HANDLER

Fomu yofunsira

Makina abwino osavuta kugwiritsa ntchito

Makina a Case TX telescopic handler ndi abwino kwambir kamba koti anawapanga moti anthu adzitha kuwagwiritsa ntchito mosavuta.

KUFIKIRA MALO APATALI

Makina amafikira mpaka pa mtunda wa ma mita khumi , asanu ndi awiri(17) ndipo ndiwodalirika kuti sangathe kugwetsa kapena kuwononga katundu.

MPHAMVU

Makina a TX Telehandler ali ndi ma engine a mphamvu omwe  samamwa mafuta kwambiri. Kupatula kuti makinawa samwa mafuta ambiri, ubwino wina ndiwoti ali ndi 516 Nm ya torque yomwe ndiyokwanira kunyamula katundu aliyense mu nyengo iliyonse. 

المواصفات :

  • Kapangidwe : TX-170-45 Turbo
  • Engine : FPT - Tier 3
  • Mphamvu : 88 kW / 118 hp
  • Kulemera (kg) : 12300