WASTE COMPACTORS

SiteID: 9
Category: C
lnggcode: ny
id:12

MAZZOCHIA SMALL SIZE COMPACTORS-MINISTAR

Ministar Single-bladed Tipper Truck: Awa amapangidwa ndi chitslo ndipo amakhala otseka; Ali ndi single blade yomwe imagwira ntchito chifkwa cha ma hydraulic cylinder ndipo imakhala bwino kunyamulira zinyalala, ma cardboard,ma plastic komanso compost.

المواصفات :

 • Volume of body: 3,5-8 mc
 • Chassis: Two axles, light
 • MTT: From 2,2 to 8 Ton

MAZZOCCHIA SMALL SIZE COMPACTORS-JOLLY 1

Compactor ya Jolly1 kuchokera pa 5 kufika pa 7m3- Makina a Monocoque omwe amakhala ndi ejection blade. Makina aang`ono a Monocoque ndiwoyenera pantchito yonyamula compost,ma pepala, ma cardboard komanso kunyamula zinthu khomo ndi khomo.

المواصفات :

 • Volume of body: 5-8 mc
 • Chassis: Two axles, light
 • MTT: From 4,5 to 8 Ton

MAZZOCCHIA MEDIUM SIZE COMPACTORS-MINIMACB

MINIMACB Compactor kuchokera pa 8 kufika pa 13 m3. Nayo MINIMACB ndi Monocoque mini-compactor ya blade imodzi yomwe imakwanitsa kuchita zinthu zambiri kamba kakuti ndi ya makoni.

المواصفات :

 • Volume of body: 8-14 mc
 • Chassis: Two axles, medium line
 • MTT: From 9 to 14 Ton

MAZZOCCHIA LARGE SIZE COMPACTORS-MAC1

Ili ndi single bladed rear-loading compactor-Mac1 ndi rear-loading compactor yomwe inapangidwira kuti izigwira ntchito zolemera. Imakhala ndi container yotseka yonyamula zinyalala komanso universal rear-hinged hopper.

المواصفات :

 • Volume of body: 26-36 mc
 • Chassis: Heavy Duty
 • MTT: 33-40 Ton

MAZZOCCHIA LARGE SIZE COMPACTORS-MAC2NB

Single bladed rear-loading compactor-Mac 2NB ndi rear-loading compactor yomwe imakhala ndi container yotseka yonyamulira zinyalala

المواصفات :

 • Volume of body: 20-25 mc
 • Chassis: 3 axles, medium-heavy line
 • MTT: 26 Ton

MAZZOCCHIA SIDE COMPACTORS-LAT2

-Side-loading single-operated compactor imakhala ndi container yosungira zinyalala yotseka komanso chonyamulira ma bin -Makinawa ali ndikuthekera konyamula zinthu zambiri pakamodzi ndipo amatha kunyamula zinyalala zolimba, ma pepala,ma galasi,ma plastic ndi masamba

المواصفات :

 • Volume of body: 15-18 mc
 • Chassis: 2 axles, medium-heavy line
 • MTT: 18 Ton

MAZZOCCHIA SIDE BIN WASHER-AQUATEC

Side-container Washer- Iyi ndi side-container yomwe imagwiritsidwa ntchito ndi munthu mmodzi pochapira mkati komanso panja pa pa container kuyambira 1800 kufikira pa 3200 litres

المواصفات :

 • Volume of body: 6.000 litres
 • Chassis: Two axle, medium line
 • MTT: 15-16 Ton

MAZZOCCHIA SIDE BIN WASHER-IDROPLUS

Rear-container Washer-Awa ndi makina ogwiritsa ntchito potsukira kunja ndi mkati mwa container yoyendayenda

المواصفات :

 • Volume of body: 6.000 litres
 • Chassis: With driver’s cab for medium line
 • MTT: 15-16 Ton