KK05

Fomu yofunsira

Awa ndi ma Generator enanso a mphamvu omwe ali ndi ma engine omwe amathanso kudziziziritsa okha
Ali ndi Thanki ya mafuta yabwino
Vibration isolators
Ma air filter abwino
Alinso ndi ma Fuel Filter abwino
Main line breaker
Batile komanso ma cable oyambiri
CPCB-certified sound encolsure

ZOPEZEKA PA ALTERNATOR 
Ndi Alternator yapamwamba kwambiri ndipo ndiyovomerezeka pa dziko lonse pankhani za ma Generator
KAMWEDWE KA MAFUTA
100% load:  1.4 Lph (0.37 gph)
75% load:  1.0 Lph (0.26 gph)
50% load:  0.7 Lph (0.18 gph)

المواصفات :

  • Prime Ratings : 4 kW (5 kVA)
  • Standby Ratings :
  • Hertz : 50 Hz
  • Alternator Type : 2-pole
  • Engine Manufacturer : Lombardini
  • Engine Model : 15LD440
  • Cylinder Arrangement : 1 Inline
  • Max Power at Rated RPM : 6.10228 kWm (8.18 BHP)