Van Yocheperapo yonyamula katundu

Fomu yofunsira

Superb technology: Tekinoloje ya mtengo wapatali imene yakhala ndi a Golden Dragon kwa zaka zoposa makumi atatu.

Electrophoretic coating: Yokutidwa mwaukadaulo ndipo inapentedwa ndi penti wosachita dzimbiri wopangidwa ku US kuti ikhale mpaka kale kale.

Robust and safe: Khoma lake ndilonkhutala kupangitsa kuti vasiyi izioneka mokongola komaso kuyenda bwino.

Elongated Body: Sichinthu chapafupi kutalikisa basi koma izi zinachitika ndicholinga choti oyikwera azikhala motakasuka. Mipando yake yaofuofu imathandiza okwera kukhala ndi ulendo wapamwamba ndipo osatopesa..

Fuel Economy: Malingana ndi makonda munthu atha kusankha basi ya petulo kapena dizilo, izi zili chonchi zimapereka mwayi malingana ndi komwe vasiyi izikayenda.

Kunena zamagwiritsidwe amafuta, mini basiyi imadziwa kusinira ndipo kuli kusankha kusankha chifukwa munthu ankhonza kugula ya petulo kapena dizilo kutengera malo amene izipita kapena dziko lomwe basiyi izikagwira ntchito.

Mini basi iyi ndiyodalirilika chifukwa isanapite pamsika inayesedwa ndi akadaulo eni eni amakonzedwe amagalimoto osiyana siyana kufuna kutsimikizira okwera kapena ogula basiyi kuti iwo sazaona mavuto ena aliwonse panthawi yomweazizagwiritsa masiyi.

Ili ndi mipando yotakasuka yopangidwa ndipo yoyalidwa 9-15 malingana ndikukonda kwa oyigula.

Mipando yotakasuka ndipo imatheka kuyisuntha kuti mukhale bwino. Imatha kunyamula anthu awiri kapena asanu.

المواصفات :

  • Mapangidwe : XML6532 - Cargo Delivery Van
  • Kukula kwake: (Mulitali x Mulifupi x Munsinkhu) mu mamilimita : 4980 × 1700 × 1980
  • Malo amatayala : 2590mm
  • Mipando : 2 - 5
  • Maziziridwe a mkati : Both Front & Rear
  • Wailesi : FM/AM Radio with Mp3 Player
  • Ingini : 4JB1 Petrol Engine ISUZU Technology
  • Mphavu ya ingine : 57KW