MINI BASI

Fomu yofunsira

Basi yayingono kutengera kukula kwake komanso kuchuluka kwa anthu imanyamula. Komatu angakhale ili yaying’ono chonchi koma basiyi ili ndi maonekedwe ake ake ndipo inapangidwa maukatswiri. Zintchito zake zilibe mzake kuonetseratu kuti a Golden Dragon anayikapo nzeru poti iwo ndiakadaulo kwa zaka zoposa makumi atatu.

Golden dragon basi ndiyopangidwa luso ndipoanthu okwera amayamikira ndimapangidwe abasi imeneyi.

Basiyi ndiyokutidwa ndi zinthu zamtengo wapatali zomwe zimaletsa dzimbiri kumanagana mkati ndi mkunja komwe, dzimbiri larephera kumanga ubale ndi basi ya Golden Dragon kwa zaka zoposa makuni awiri.

Pa mibado isanu ndi umodzi PPG yakhala ikuthandiza kuonetsetsa kuti ma basiwa ndiolimba komatso owalamochitisa kaso.

Kunena mwatchutchutchu ma mini basiwa anapangidwa kuti okwera akhale otakasuka ndipo ndiokhutala bwino komaso ndiodalirika pa ulendo wanu.

Saizi ya basiyi inaonjezedwa kuti mkatimo mukhale kutakasuka ndipo kunena za mipando yake imakhalangati ya mundenge kupereka chisangalalo kwa onse apaulendo.

Nkhope ya mini basiyi yapasidwa nkhope yanyuwani kuonjezera kukongola kwa basiyi.

Kunena zamagwiritsidwe amafuta, mini basiyi imadziwa kusinira ndipo kuli kusankha kusankha chifukwa munthu ankhonza kugula ya petulo kapena dizilo kutengera malo amene izipita kapena dziko lomwe basiyi izikagwira ntchito.

Mini basi iyi ndiyodalirilika chifukwa isanapite pamsika inayesedwa ndi akadaulo eni eni amakonzedwe amagalimoto osiyana siyana kufuna kutsimikizira okwera kapena ogula basiyi kuti iwo sazaona mavuto ena aliwonse panthawi yomweazizagwiritsa masiyi.

Ili ndi mipando yotakasuka yopangidwa ndipo yoyalidwa 9-15 malingana ndikukonda kwa oyigula.

المواصفات :

  • Mapangidwe : XML6500J2
  • Kukula kwake: (Mulitali x Mulifupi x Munsinkhu) mu mamilimita : 4980 × 1700 × 1980
  • Malo amatayala : 2590mm
  • Mipando : 12-15
  • Maziziridwe a mkati : Both Front & Rear
  • Wailesi : FM/AM Radio with Mp3 Player
  • Ingini : JM491Q-ME Petrol Engine Toyota Technology - Euro III
  • Mphavu ya ingine : 75KW