BASI YOYENDA MAULENDO ATALI ATALI kapena kuti City to City

Fomu yofunsira

Basi iyi ya Interciry yomwe ndiyopangidwa mwapadera kuti iziyenda maulendo aatali atali ndipo ili ndi injini ya mtundu wa XML6117 yomwe imakhala kutsogolo kwabasi. Kubwedzeretsedwa kwa injini poyika kutsogolo ngati momwe zinaliri kale kale ndikotchuka chifukwa basi imayenda bwino malingana ndikunena kwa opanga basiyi a Golden Dragon.

Xml6117 ndi injiniyokhala kutsogolo kwa basi, iyi ndi njira ya makezana kuma yondalirika kwambiri chifukwa basi imayenda bwino malingana ndikunena kwa a Golden Dragon.

المواصفات :

  • Mapangidwe : XML6117J12
  • Kukula kwake: (Mulitali x Mulifupi x Munsinkhu) mu mamilimita : 11605 × 2500 × 3710
  • Malo amatayala : 5800 mm
  • Mipando : 61 (60+1)
  • Maziziridwe a mkati : 28,000 to 30,000Kcal/Hr
  • Wailesi : DVD Player with 19" LCD Monitor
  • Ingini : Cummins L300-20 Six Cylinder
  • Mphavu ya ingine : 221KW /2200rpm