MA BASI

SiteID: 9
Category: C
lnggcode: ny
id:15

MINI BUS

Golden Dragon basi ndi basi yopangidwa mwapadera and ili ndi tekinoloje yapamwamba kuti izigwirizana ndizofuna za anthu ogula ndi ogwiritsa ntchito basiyi. Mabasi a Golden Dragon akhala akupangidwa ndi luso lapamwambali kwa zaka zoposa makumi awiri.

المواصفات :

 • Mapangidwe: XML6500J2
 • Kukula kwake: (Mulitali x Mulifupi x Munsinkhu) mu mamilimita: 4980 × 1700 × 1980
 • Malo amatayala: 2590mm
 • Mipando: 12-15
 • Maziziridwe a mkati: Both Front & Rear
 • Wailesi: FM/AM Radio with Mp3 Player
 • Ingini: 4JB1 Diesel Engine ISUZU Technology
 • Mphavu ya ingine: 57KW

KOCHI YAMANYADO YOCHEPERAPO

Kochi yocheperapoyi ndi yaofuofu ndipo ikungodikira inu mukaone ndikuvomereza kuti apa panagona luso.Basiyi iliphuliphuli kuchitira umboni zaubwino wake.

المواصفات :

 • Mapangidwe: XML6857J12
 • Kukula kwake: (Mulitali x Mulifupi x Munsinkhu) mu mamilimita: L8540 × W2500 × H3300
 • Malo amatayala:
 • Mipando: 35
 • Maziziridwe a mkati: 28,000 Kcal/Hr
 • Wailesi: DVD Player with 17" LCD Monitor
 • Ingini: Cummins EQB210-20 - Diesel Engine
 • Mphavu ya ingine: 155Kw/2500rpm

BASI YOYENDA MAULENDO ATALI ATALI kapena kuti City to City

Basi iyi ya Interciry yomwe ndiyopangidwa mwapadera kuti iziyenda maulendo aatali atali ndipo ili ndi injini ya mtundu wa XML6117 yomwe imakhala kutsogolo kwabasi. Kubwedzeretsedwa kwa injini poyika kutsogolo ngati momwe zinaliri kale kale ndikotchuka chifukwa basi imayenda bwino malingana ndikunena kwa opanga basiyi a Golden Dragon.

المواصفات :

 • Mapangidwe: XML6117J12
 • Kukula kwake: (Mulitali x Mulifupi x Munsinkhu) mu mamilimita: 11605 × 2500 × 3710
 • Malo amatayala: 5800 mm
 • Mipando: 61 (60+1)
 • Maziziridwe a mkati: 28,000 to 30,000Kcal/Hr
 • Wailesi: DVD Player with 19" LCD Monitor
 • Ingini: Cummins L300-20 Six Cylinder
 • Mphavu ya ingine: 221KW /2200rpm

LUXURY COACH BUS

Mtundu wa XML6122 ndi basi yopangidwa ndimaulemu apadera okhala ndimizere yokongola ndipo yopangidwa bwino. Maonekedwe ochitisa kasowa anatengera ku Ulaya ndi mayiko ena akumvuma. Luxury Coach imapangidwa ku China ndi a Golden Dragon.

المواصفات :

 • Mapangidwe: XML6122J13
 • Kukula kwake: (Mulitali x Mulifupi x Munsinkhu) mu mamilimita: 12000 × 2550 × 3690
 • Malo amatayala: 6000 mm
 • Mipando: 51 (49+1+1)
 • Maziziridwe a mkati: Songz 32,000Kcal/Hr
 • Wailesi: DVD Player with 2 Nos 22" & 19" LCD Monitors
 • Ingini: Cummins Diesel Engine -ISLe 340 30 Six Cylinder
 • Mphavu ya ingine: 250KW /2100rpm

MINI BASI

Basi yayingono kutengera kukula kwake komanso kuchuluka kwa anthu imanyamula. Komatu angakhale ili yaying’ono chonchi koma basiyi ili ndi maonekedwe ake ake ndipo inapangidwa maukatswiri.

المواصفات :

 • Mapangidwe: XML6500J2
 • Kukula kwake: (Mulitali x Mulifupi x Munsinkhu) mu mamilimita: 4980 × 1700 × 1980
 • Malo amatayala: 2590mm
 • Mipando: 12-15
 • Maziziridwe a mkati: Both Front & Rear
 • Wailesi: FM/AM Radio with Mp3 Player
 • Ingini: JM491Q-ME Petrol Engine Toyota Technology - Euro III
 • Mphavu ya ingine: 75KW

Van Yocheperapo yonyamula katundu

A Golden Dragon anapungulira ukadaulo womwe anapangira Golden Dragon Bus ku Mini Delivery Van. Tekinolje yonse ya zakamakumi awiri yonse ili pa Van imeneyi.

المواصفات :

 • Mapangidwe: XML6532 - Cargo Delivery Van
 • Kukula kwake: (Mulitali x Mulifupi x Munsinkhu) mu mamilimita: 4980 × 1700 × 1980
 • Malo amatayala: 2590mm
 • Mipando: 2 - 5
 • Maziziridwe a mkati: Both Front & Rear
 • Wailesi: FM/AM Radio with Mp3 Player
 • Ingini: 4JB1 Petrol Engine ISUZU Technology
 • Mphavu ya ingine: 57KW

Van Yocheperapo yonyamula katundu

A Golden Dragon anapungulira ukadaulo womwe anapangira Golden Dragon Bus ku Mini Delivery Van. Tekinolje yonse ya zakamakumi awiri yonse ili pa Van imeneyi.

المواصفات :

 • Mapangidwe: XML6532 - Cargo Delivery Van
 • Kukula kwake: (Mulitali x Mulifupi x Munsinkhu) mu mamilimita: 4980 × 1700 × 1980
 • Malo amatayala: 2590mm
 • Mipando: 2 - 5
 • Maziziridwe a mkati: Both Front & Rear
 • Wailesi: FM/AM Radio with Mp3 Player
 • Ingini: 4JB1 Diesel Engine ISUZU Technology
 • Mphavu ya ingine: 57KW

BASI YOCHEPERAPO

Pakadali pano Golden DragonXML6722J18 yaonjezera kutalika kwa basi yakre pokhala ndi mipando 31 ndipo ikuyendera enjini yamtundun wa 3.8L. Basiyi tikayifananiza ndi mabsai ena omwe ali pansika kale tiona kuti iyo ikutsogola kwambiri pazichito chito zake monga, kunyamula anthu ochuluka komanso kukhala omasuka.

المواصفات :

 • Mapangidwe: XML6722J18
 • Kukula kwake: (Mulitali x Mulifupi x Munsinkhu) mu mamilimita: 7245 × 2280 × 2960
 • Malo amatayala: 3935 mm
 • Mipando: 30 (27+2+1)
 • Maziziridwe a mkati: Both Front & Rear
 • Wailesi: FM/AM Radio with Mp3 Player
 • Ingini: Cummins Diesel Engine - ISF 3.8
 • Mphavu ya ingine: 105KW /2600rpm

LUXURY COACH BUS

Mtundu wa XML6125J12 ndi basi yopangidwa ndimaulemu apadera okhala ndimizere yokongola ndipo yopangidwa bwino.

المواصفات :

 • Mapangidwe: XML6125J12
 • Kukula kwake: (Mulitali x Mulifupi x Munsinkhu) mu mamilimita: 12000 × 2550 × 3690
 • Malo amatayala: 6000 mm
 • Mipando: 51 (49+1+1)
 • Maziziridwe a mkati: Songz 32,000Kcal/Hr
 • Wailesi: DVD Player with 2 Nos 22" & 19" LCD Monitors
 • Ingini: Cummins Diesel Engine -ISLe 340 30 Six Cylinder
 • Mphavu ya ingine: 250KW /2100rpm

MABASI OZUNGULIRA MTAUNI

Kukula kwa ma basi awa kumapangitsa kuti mkati mwake mukhale motakasuka ndiponso mowala. Basiyi ili ndi zitseko zazikulu zomwe zimathandiza kuti anthu athe ku kwera kapena ku tsika mosavuta panthawi yomwe iwo akufulumira.

المواصفات :

 • Mapangidwe: XML6125J13C
 • Kukula kwake: (Mulitali x Mulifupi x Munsinkhu) mu mamilimita: 12000×2500×3350
 • Malo amatayala: 6100 mm
 • Mipando: 122(34+2+1+85 Standing)122(34+2+1+85 Standing)
 • Maziziridwe a mkati: 30,000Kcal/hr
 • Wailesi: FM/AM Radio with Mp3 Player
 • Ingini: CUMMINS ISLe 310 31 - Diesel
 • Mphavu ya ingine: 228kW/2200rpm