Lombardini

Lombardin s.r.1 ndi kampani ya mdziko la Italy yomwe imapanga ma Engine a Dizilo ofika mpaka pa 65hp. Kampaniyi inayambitsidwa ndi Adelmo komanso Rainero Lombardini ku Reggio Emilia mchaka cha 1933. Poyambilira kampaniyi imkatchuka ndi dzina lokuti Fabbrica Italiana Motori S.P.A

Available in