Iveco

Kampani ya Iveco ili ndi galimoto zikuluzikulu za mtundu wa Truck zosiyanasiyana. Galimotozi zimapangidwa molingana ndi kufunikira kwake,ntchito kapena zolinga zogwiritsira ntchito  komanso dera lomwe galimotoyo idzikayenda. Kampani ya Iveco ndiyokhayo yayikulu kwambiri pantchito yopanga galimoto zikulu-zikulu komanso ma Van. Galimoto za Iveco ndi zodallirika ndipo zimagwira ntchito mu dera lirilonse mosawona kulemera kwa katundu kapena malo amene katunduyoakupita. Kampani-yi imapezekanso kwambiri ku dera la Africa komanso ku mayiko a chiluya.

Kampani ya Iveco ikupezeka mzigawo za:

  • UAE¬† komanso GCC
  • Africa

Available in